-
Yeremiya 44:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Choncho Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Ine ndatsimikiza kukugwetserani tsoka, kuti ndiwononge anthu onse a mu Yuda.
-