-
Yeremiya 44:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Ndipo anthu otsala a ku Yuda amene apita kukakhala mʼdziko la Iguputo sadzathawa kapena kupulumuka kuti abwerere kudziko la Yuda. Adzafunitsitsa kubwerera kuti akakhale kumeneko koma sadzabwerera kupatulapo anthu ochepa amene adzathawe.’”
-