Yeremiya 44:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Ndipotu kungoyambira nthawi imene tinasiya kupereka nsembe ndi kuthira nsembe zachakumwa kwa Mfumukazi Yakumwamba,* tikusowa chilichonse ndipo tawonongeka ndi lupanga komanso njala.” Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 44:18 Nsanja ya Olonda,5/15/1999, ptsa. 13-14
18 Ndipotu kungoyambira nthawi imene tinasiya kupereka nsembe ndi kuthira nsembe zachakumwa kwa Mfumukazi Yakumwamba,* tikusowa chilichonse ndipo tawonongeka ndi lupanga komanso njala.”