Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yeremiya 44:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Mulungu wa Isiraeli, wanena kuti, ‘Zimene inu ndi akazi anu mwanena mwazikwaniritsadi ndi manja anu chifukwa munanena kuti: “Ife tidzakwaniritsa malonjezo athu akuti tidzapereka nsembe kwa Mfumukazi Yakumwamba* ndi kuti tidzapereka nsembe yachakumwa kwa iye.”+ Akazi inu muchitadi zimene mwalonjeza ndipo mukwaniritsadi malonjezo anu.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena