Yeremiya 44:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Ine ndine wokonzeka kuwabweretsera tsoka, osati zinthu zabwino.+ Anthu onse a ku Yuda amene ali mʼdziko la Iguputo adzafa ndi lupanga ndiponso njala mpaka atatheratu.+
27 Ine ndine wokonzeka kuwabweretsera tsoka, osati zinthu zabwino.+ Anthu onse a ku Yuda amene ali mʼdziko la Iguputo adzafa ndi lupanga ndiponso njala mpaka atatheratu.+