-
Yeremiya 44:29Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
29 “Yehova wanena kuti: ‘Ndikupatsani chizindikiro chosonyeza kuti ndidzakulangani mʼdziko lino kuti mudziwe kuti mawu anga akuti ndidzakubweretserani tsoka adzakwaniritsidwadi.
-