-
Yeremiya 44:30Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
30 Yehova wanena kuti: “Ine ndikupereka Farao Hofira, mfumu ya Iguputo, mʼmanja mwa adani ake ndiponso mʼmanja mwa amene akufuna kuchotsa moyo wake, mofanana ndi mmene ndinaperekera Zedekiya mfumu ya Yuda mʼmanja mwa Nebukadinezara* mfumu ya Babulo, amene anali mdani wake komanso amene ankafuna kumupha.”’”+
-