Yeremiya 46:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Mitundu ya anthu yamva zochititsa manyazi zimene zakuchitikira,+Ndipo kulira kwako kwamveka mʼdziko lonse. Asilikali apunthwitsana,Ndipo onse agwera limodzi.”
12 Mitundu ya anthu yamva zochititsa manyazi zimene zakuchitikira,+Ndipo kulira kwako kwamveka mʼdziko lonse. Asilikali apunthwitsana,Ndipo onse agwera limodzi.”