Yeremiya 46:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 “Lengezani zimenezi mu Iguputo, muzilengeze ku Migidoli.+ Lengezani zimenezi ku Nofi* ndi ku Tahapanesi.+ Munene kuti, ‘Imani mʼmalo anu ndipo mukhale okonzeka,Chifukwa lupanga lidzawononga anthu onse amene akuzungulirani.
14 “Lengezani zimenezi mu Iguputo, muzilengeze ku Migidoli.+ Lengezani zimenezi ku Nofi* ndi ku Tahapanesi.+ Munene kuti, ‘Imani mʼmalo anu ndipo mukhale okonzeka,Chifukwa lupanga lidzawononga anthu onse amene akuzungulirani.