Yeremiya 46:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 ‘Iye akuchita phokoso ngati la njoka imene ikuthamanga,Chifukwa adaniwo amufikira mwamphamvu, atatenga nkhwangwa,Ngati amuna amene akukagwetsa mitengo.* Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 46:22 Nsanja ya Olonda,3/15/2007, tsa. 11
22 ‘Iye akuchita phokoso ngati la njoka imene ikuthamanga,Chifukwa adaniwo amufikira mwamphamvu, atatenga nkhwangwa,Ngati amuna amene akukagwetsa mitengo.*