-
Yeremiya 46:23Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
23 Iwo adzadula nkhalango yake ngakhale kuti ndi yowirira,’ akutero Yehova.
‘Chifukwa adaniwo ndi ochuluka kwambiri kuposa dzombe ndipo ndi osawerengeka.
-