Yeremiya 48:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Mowabu sakutamandidwanso. Ku Hesiboni+ adani amukonzera chiwembu kuti amuwononge ndipo akunena kuti: ‘Bwerani, tiyeni timuwononge kuti asakhalenso mtundu wa anthu.’ Iwenso Madimeni khala chete,Chifukwa lupanga likukutsatira.
2 Mowabu sakutamandidwanso. Ku Hesiboni+ adani amukonzera chiwembu kuti amuwononge ndipo akunena kuti: ‘Bwerani, tiyeni timuwononge kuti asakhalenso mtundu wa anthu.’ Iwenso Madimeni khala chete,Chifukwa lupanga likukutsatira.