Yeremiya 48:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Chifukwa chakuti mukudalira ntchito zanu ndi chuma chanu,Inunso mudzagwidwa ndi adani. Ndipo Kemosi+ adzatengedwa kupita ku ukapoloPamodzi ndi ansembe ake ndi akalonga ake.
7 Chifukwa chakuti mukudalira ntchito zanu ndi chuma chanu,Inunso mudzagwidwa ndi adani. Ndipo Kemosi+ adzatengedwa kupita ku ukapoloPamodzi ndi ansembe ake ndi akalonga ake.