-
Yeremiya 48:11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
11 Anthu a ku Mowabu akhala popanda wowasokoneza kuyambira pa unyamata wawo
Ngati vinyo amene nsenga zake zadikha.
Iwo sanatsanulidwepo kuchoka mʼchiwiya china kupita mʼchiwiya china,
Ndipo sanapitepo ku ukapolo.
Nʼchifukwa chake kukoma kwawo sikunasinthe,
Ndipo fungo lawo silinasinthenso.
-