Yeremiya 48:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Tsika pamalo ako aulemereroNdipo ukhale pansi uli ndi ludzu,* iwe mwana wamkazi wokhala ku Diboni+Chifukwa wowononga Mowabu wabwera kudzakuukira,Ndipo malo ako a mipanda yolimba kwambiri adzawasandutsa bwinja.+
18 Tsika pamalo ako aulemereroNdipo ukhale pansi uli ndi ludzu,* iwe mwana wamkazi wokhala ku Diboni+Chifukwa wowononga Mowabu wabwera kudzakuukira,Ndipo malo ako a mipanda yolimba kwambiri adzawasandutsa bwinja.+