Yeremiya 48:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Kerioti,+ Bozira ndi mizinda yonse yamʼdziko la Mowabu, yakutali ndi yapafupi.