Yeremiya 48:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 ‘Muledzeretseni+ chifukwa wadzikuza pamaso pa Yehova.+ Mowabu akugubuduka mʼmasanzi ake,Ndipo wakhala chinthu choyenera kuchinyoza.
26 ‘Muledzeretseni+ chifukwa wadzikuza pamaso pa Yehova.+ Mowabu akugubuduka mʼmasanzi ake,Ndipo wakhala chinthu choyenera kuchinyoza.