Yeremiya 48:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kodi kwa inu, Isiraeli sanali chinthu choyenera kunyozedwa?+ Kodi anapezeka pakati pa anthu akuba,Kuti inu mumupukusire mitu nʼkumamunenera zinthu zoipa?
27 Kodi kwa inu, Isiraeli sanali chinthu choyenera kunyozedwa?+ Kodi anapezeka pakati pa anthu akuba,Kuti inu mumupukusire mitu nʼkumamunenera zinthu zoipa?