-
Yeremiya 48:28Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
28 Inu anthu okhala ku Mowabu, chokani mʼmizinda ndipo mukakhale pathanthwe.
Mukhale ngati njiwa imene imamanga chisa chake mʼmbali mwa khomo la phanga.’”
-