-
Yeremiya 48:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
Ndachititsa kuti vinyo asiye kutuluka moponderamo mphesa.
Palibe amene adzapondeponde mphesa akufuula mosangalala.
Padzamveka kufuula koma osati kwachisangalalo.’”+
-