Yeremiya 48:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Yehova wanena kuti: ‘Taonani! Mofanana ndi chiwombankhanga chimene chimatsika nʼkugwira chakudya chake,+Mdani adzatambasula mapiko ake nʼkugwira Mowabu.+
40 Yehova wanena kuti: ‘Taonani! Mofanana ndi chiwombankhanga chimene chimatsika nʼkugwira chakudya chake,+Mdani adzatambasula mapiko ake nʼkugwira Mowabu.+