-
Yeremiya 48:41Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
41 Matauni adzalandidwa,
Ndipo malo ake otetezeka adzalandidwa.
Pa tsiku limenelo, mitima ya asilikali a ku Mowabu
Idzakhala ngati mtima wa mkazi amene akubereka.
-