Yeremiya 48:42 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 42 Mowabu adzawonongedwa ndipo sadzakhalanso mtundu wa anthu,+Chifukwa wadzikweza pamaso pa Yehova.+