Yeremiya 48:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Tsoka iwe Mowabu! Anthu a Kemosi+ awonongedwa. Ana ako aamuna agwidwa ndi adani,Ndipo ana ako aakazi atengedwa kupita kudziko lina.+
46 Tsoka iwe Mowabu! Anthu a Kemosi+ awonongedwa. Ana ako aamuna agwidwa ndi adani,Ndipo ana ako aakazi atengedwa kupita kudziko lina.+