Yeremiya 48:47 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 47 Koma mʼmasiku otsiriza ine ndidzasonkhanitsa Amowabu onse amene anagwidwa nʼkutengedwa kupita kudziko lina,’ akutero Yehova. ‘Apa ndi pamene pathera chiweruzo chokhudza Mowabu.’”+
47 Koma mʼmasiku otsiriza ine ndidzasonkhanitsa Amowabu onse amene anagwidwa nʼkutengedwa kupita kudziko lina,’ akutero Yehova. ‘Apa ndi pamene pathera chiweruzo chokhudza Mowabu.’”+