Yeremiya 49:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Ponena za Edomu, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Kodi nzeru zinatha ku Temani?+ Kodi anthu ozindikira sakuperekanso malangizo anzeru? Kodi nzeru zawo zinawola?
7 Ponena za Edomu, Yehova wa magulu ankhondo akumwamba wanena kuti: “Kodi nzeru zinatha ku Temani?+ Kodi anthu ozindikira sakuperekanso malangizo anzeru? Kodi nzeru zawo zinawola?