Yeremiya 49:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Thawani! Bwererani! Pitani kumalo otsika kuti mukakhale kumeneko, inu amene mukukhala ku Dedani!+ Chifukwa Esau ndidzamugwetsera tsokaNthawi yoti ndimupatse chilango ikadzafika.
8 Thawani! Bwererani! Pitani kumalo otsika kuti mukakhale kumeneko, inu amene mukukhala ku Dedani!+ Chifukwa Esau ndidzamugwetsera tsokaNthawi yoti ndimupatse chilango ikadzafika.