Yeremiya 49:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Yehova wanena kuti: “Taonani! Ngati amene sanapatsidwe chiweruzo kuti amwe zamʼkapu akuyenera kumwa, kodi iweyo ukuyenera kusiyidwa osapatsidwa chilango? Ayi, sudzasiyidwa osapatsidwa chilango chifukwa ukuyenera kumwa zamʼkapumo.”+
12 Yehova wanena kuti: “Taonani! Ngati amene sanapatsidwe chiweruzo kuti amwe zamʼkapu akuyenera kumwa, kodi iweyo ukuyenera kusiyidwa osapatsidwa chilango? Ayi, sudzasiyidwa osapatsidwa chilango chifukwa ukuyenera kumwa zamʼkapumo.”+