-
Yeremiya 49:16Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
16 Iwe unachititsa kuti anthu azinjenjemera ndipo zimenezi zakupusitsa,
Mtima wako wodzikuza wakupusitsa,
Iwe amene ukukhala mʼmalo obisika amʼthanthwe,
Amene ukukhala paphiri lalitali kwambiri.
Ngakhale kuti unamanga chisa chako pamwamba kwambiri ngati chiwombankhanga,
Ine ndidzakugwetsa kuchoka pamenepo,” akutero Yehova.
-