Yeremiya 49:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 “Edomu adzakhala chinthu chochititsa mantha.+ Aliyense wodutsa pafupi naye adzamuyangʼanitsitsa mwamantha nʼkumuimbira mluzu chifukwa cha miliri yonse imene idzamugwere. Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 49:17 Yeremiya, tsa. 163 Kukambitsirana, tsa. 55
17 “Edomu adzakhala chinthu chochititsa mantha.+ Aliyense wodutsa pafupi naye adzamuyangʼanitsitsa mwamantha nʼkumuimbira mluzu chifukwa cha miliri yonse imene idzamugwere.