Yeremiya 49:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Mofanana ndi mmene Sodomu ndi Gomora komanso midzi imene anali nayo pafupi inawonongedwera, ndi mmenenso zidzakhalire ndi Edomu.+ Palibe aliyense amene adzakhalenso mʼdzikolo,” akutero Yehova.+ Yeremiya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 49:18 Yeremiya, tsa. 163 Kukambitsirana, tsa. 55
18 Mofanana ndi mmene Sodomu ndi Gomora komanso midzi imene anali nayo pafupi inawonongedwera, ndi mmenenso zidzakhalire ndi Edomu.+ Palibe aliyense amene adzakhalenso mʼdzikolo,” akutero Yehova.+