20 Tsopano amuna inu, tamverani zimene Yehova wasankha kuchitira Edomu ndiponso zimene waganiza kuti achitire anthu amene akukhala ku Temani:+
Ndithudi, chilombo chidzakokera kutali ana a nkhosa.
Adzachititsa kuti malo awo okhala asanduke bwinja chifukwa cha zimene anthuwo anachita.+