Yeremiya 49:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Taonani! Mofanana ndi chiwombankhanga mdani adzatsika nʼkugwira chakudya chake,+Ndipo adzatambasula mapiko ake pa Bozira.+ Pa tsiku limenelo mtima wa asilikali a ku EdomuUdzakhala ngati mtima wa mkazi amene akubereka.”
22 Taonani! Mofanana ndi chiwombankhanga mdani adzatsika nʼkugwira chakudya chake,+Ndipo adzatambasula mapiko ake pa Bozira.+ Pa tsiku limenelo mtima wa asilikali a ku EdomuUdzakhala ngati mtima wa mkazi amene akubereka.”