Yeremiya 49:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Uthenga wokhudza Damasiko ndi wakuti:+ “Hamati+ ndi Aripadi achititsidwa manyaziChifukwa chakuti amva uthenga woipa. Iwo agwidwa ndi mantha aakulu. Nyanja yachita mafunde ndipo singathe kukhala bata.
23 Uthenga wokhudza Damasiko ndi wakuti:+ “Hamati+ ndi Aripadi achititsidwa manyaziChifukwa chakuti amva uthenga woipa. Iwo agwidwa ndi mantha aakulu. Nyanja yachita mafunde ndipo singathe kukhala bata.