-
Yeremiya 49:24Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
24 Damasiko sanathenso kulimba mtima.
Watembenuka kuti athawe koma wagwidwa ndi mantha aakulu.
Iye wagwidwa ndi nkhawa ndiponso zowawa,
Ngati mkazi amene akubereka.
-