-
Yeremiya 49:26Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
26 Chifukwa anyamata ake adzaphedwa mʼmabwalo ake,
Ndipo asilikali onse adzaphedwa tsiku limenelo,” akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba.
-