Yeremiya 49:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Ponena za Kedara+ ndi maufumu a ku Hazori amene Mfumu Nebukadinezara* ya Babulo inawagonjetsa, Yehova wanena kuti: “Nyamukani, pitani ku Kedara,Ndipo mukawononge ana a Kumʼmawa.
28 Ponena za Kedara+ ndi maufumu a ku Hazori amene Mfumu Nebukadinezara* ya Babulo inawagonjetsa, Yehova wanena kuti: “Nyamukani, pitani ku Kedara,Ndipo mukawononge ana a Kumʼmawa.