Yeremiya 49:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 “Thawani, pitani kutali. Pitani ndipo mukakhale mʼmalo otsika, inu anthu amene mukukhala ku Hazori,” akutero Yehova. “Chifukwa Nebukadinezara* mfumu ya Babulo wakonza njira yoti akuukireni,Ndipo wakonza pulani kuti akugonjetseni.”
30 “Thawani, pitani kutali. Pitani ndipo mukakhale mʼmalo otsika, inu anthu amene mukukhala ku Hazori,” akutero Yehova. “Chifukwa Nebukadinezara* mfumu ya Babulo wakonza njira yoti akuukireni,Ndipo wakonza pulani kuti akugonjetseni.”