-
Yeremiya 49:31Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
31 “Nyamukani, pitani mukaukire mtundu wa anthu umene ukukhala mwamtendere,
Umene ukukhala popanda chosokoneza!” akutero Yehova.
“Kumeneko kulibe zitseko ndi mipiringidzo. Anthu ake amakhala kwaokhaokha.
-