-
Yeremiya 49:33Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
33 “Hazori adzakhala malo obisalamo mimbulu,
Adzakhala bwinja mpaka kalekale.
Palibe munthu amene adzakhale kumeneko,
Ndipo palibe aliyense amene adzakhazikike kumeneko.”
-