-
Yeremiya 49:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Anthu a ku Elamu ndidzawabweretsera mphepo 4 kuchokera kumalekezero 4 akumwamba, ndipo ndidzawabalalitsira kumphepo zonsezi. Sipadzapezeka mtundu wa anthu kumene anthu a ku Elamu amene abalalitsidwa sadzapitako.’”
-