Yeremiya 50:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Adani awo akawapeza, akumawadya+ ndipo akumanena kuti, ‘Ife tilibe mlandu uliwonse, chifukwa iwo anachimwira Yehova, malo amene chilungamo chimakhalamo. Anachimwira Yehova, chiyembekezo cha makolo awo.’”
7 Adani awo akawapeza, akumawadya+ ndipo akumanena kuti, ‘Ife tilibe mlandu uliwonse, chifukwa iwo anachimwira Yehova, malo amene chilungamo chimakhalamo. Anachimwira Yehova, chiyembekezo cha makolo awo.’”