Yeremiya 50:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Thawani mʼBabulo,Tulukani mʼdziko la Akasidi,+Ndipo mukhale ngati mbuzi kapena nkhosa zamphongo zimene zikutsogolera gulu lonse.
8 “Thawani mʼBabulo,Tulukani mʼdziko la Akasidi,+Ndipo mukhale ngati mbuzi kapena nkhosa zamphongo zimene zikutsogolera gulu lonse.