Yeremiya 50:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova, mʼdzikomo simudzakhalanso anthu.+Dziko lonselo lidzakhala bwinja.+ Aliyense wodutsa pafupi ndi Babulo adzayangʼanitsitsa mwamanthaNdipo adzamuimbira mluzu chifukwa cha miliri yake yonse.+
13 Chifukwa cha mkwiyo wa Yehova, mʼdzikomo simudzakhalanso anthu.+Dziko lonselo lidzakhala bwinja.+ Aliyense wodutsa pafupi ndi Babulo adzayangʼanitsitsa mwamanthaNdipo adzamuimbira mluzu chifukwa cha miliri yake yonse.+