Yeremiya 50:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mufuulireni mfuu yankhondo kuchokera kumbali zonse. Iye wavomereza kuti wagonja.* Zipilala zake zagwa, mipanda yake yagwetsedwa,+Chifukwa Yehova akumubwezera.+ Inunso mubwezereni. Muchitireni zimene iye anakuchitirani.+
15 Mufuulireni mfuu yankhondo kuchokera kumbali zonse. Iye wavomereza kuti wagonja.* Zipilala zake zagwa, mipanda yake yagwetsedwa,+Chifukwa Yehova akumubwezera.+ Inunso mubwezereni. Muchitireni zimene iye anakuchitirani.+