Yeremiya 50:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 “Pitani mukaukire dziko la Merataimu komanso anthu amene akukhala ku Pekodi.+ Iphani anthu onse nʼkuwawonongeratu,” akutero Yehova. “Chitani zonse zimene ndakulamulani.
21 “Pitani mukaukire dziko la Merataimu komanso anthu amene akukhala ku Pekodi.+ Iphani anthu onse nʼkuwawonongeratu,” akutero Yehova. “Chitani zonse zimene ndakulamulani.