Yeremiya 50:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iwe Babulo ndinakutchera msampha ndipo wakodwa,Koma iwe sunadziwe. Unapezeka ndi kugwidwa,+Chifukwa unkalimbana ndi Yehova.
24 Iwe Babulo ndinakutchera msampha ndipo wakodwa,Koma iwe sunadziwe. Unapezeka ndi kugwidwa,+Chifukwa unkalimbana ndi Yehova.