Yeremiya 50:31 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 31 “Taona! Ine ndikupatsa chilango,+ iwe Babulo wodzikuza,”+ akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa.“Chifukwa tsiku lako lifika, nthawi imene ndikuyenera kukupatsa chilango.
31 “Taona! Ine ndikupatsa chilango,+ iwe Babulo wodzikuza,”+ akutero Yehova wa magulu ankhondo akumwamba, Ambuye Wamkulu Koposa.“Chifukwa tsiku lako lifika, nthawi imene ndikuyenera kukupatsa chilango.