45 Tsopano amuna inu, tamverani zimene Yehova wasankha kuchitira Babulo+ ndiponso zimene waganiza kuti achitire dziko la Akasidi.
Ndithudi, chilombo chidzakokera kutali ana a nkhosa.
Adzachititsa kuti malo awo okhala asanduke bwinja chifukwa cha zimene anthuwo anachita.+