Yeremiya 51:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ine ndidzatumiza anthu opeta ku Babulo,Ndipo adzamupeta nʼkusiya dziko lake lili lopanda kanthu.Pa tsiku la tsoka lake, anthuwo adzamuukira kuchokera kumbali zonse.+
2 Ine ndidzatumiza anthu opeta ku Babulo,Ndipo adzamupeta nʼkusiya dziko lake lili lopanda kanthu.Pa tsiku la tsoka lake, anthuwo adzamuukira kuchokera kumbali zonse.+